Salimo 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Moyo wanga ukulakalaka Mulungu,+ ukulakalaka Mulungu wamoyo.+Ndidzapita liti kunyumba ya Mulungu kukaonekera pamaso pake?+ Salimo 84:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndimalakalaka mabwalo a Yehova ndipo ndafookeratu chifukwa cholakalaka mabwalowo.+Mtima wanga ndi thupi langa zikufuula mosangalala kwa Mulungu wamoyo.+ Yesaya 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Usiku, mtima wanga umakulakalakani.+ Ndithu ndimakufunafunani ndi mtima wonse,+ chifukwa mukadzaweruza dziko lapansi,+ anthu okhala panthaka ya dzikolo adzaphunzira chilungamo.+
2 Moyo wanga ukulakalaka Mulungu,+ ukulakalaka Mulungu wamoyo.+Ndidzapita liti kunyumba ya Mulungu kukaonekera pamaso pake?+
2 Ndimalakalaka mabwalo a Yehova ndipo ndafookeratu chifukwa cholakalaka mabwalowo.+Mtima wanga ndi thupi langa zikufuula mosangalala kwa Mulungu wamoyo.+
9 Usiku, mtima wanga umakulakalakani.+ Ndithu ndimakufunafunani ndi mtima wonse,+ chifukwa mukadzaweruza dziko lapansi,+ anthu okhala panthaka ya dzikolo adzaphunzira chilungamo.+