Ekisodo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+ Deuteronomo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inuyo mukudziwa bwino lero, (sindikulankhulatu ndi ana anu amene sanadziwe ndi kuona chilango* cha Yehova+ Mulungu wanu, ukulu wake+ ndi dzanja lake lamphamvu+ ndi mkono wake wotambasula,+ Salimo 145:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Ndipo ukulu wake ndi wosasanthulika.+ Yeremiya 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu mumasonyeza anthu masauzande ambiri kukoma mtima kosatha.+ Mumabwezera zolakwa za abambo kwa ana awo.*+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu+ ndi wamphamvu,+ ndipo dzina lanu+ ndinu Yehova wa makamu.+
6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+
2 Inuyo mukudziwa bwino lero, (sindikulankhulatu ndi ana anu amene sanadziwe ndi kuona chilango* cha Yehova+ Mulungu wanu, ukulu wake+ ndi dzanja lake lamphamvu+ ndi mkono wake wotambasula,+
18 Inu mumasonyeza anthu masauzande ambiri kukoma mtima kosatha.+ Mumabwezera zolakwa za abambo kwa ana awo.*+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu+ ndi wamphamvu,+ ndipo dzina lanu+ ndinu Yehova wa makamu.+