Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mulungu anamuyankha Mose kuti: “NDIDZAKHALA AMENE NDIDZAFUNE KUKHALA.”+ Ndiyeno anawonjezera kuti: “Ana a Isiraeli ukawauze kuti, ‘NDIDZAKHALA AMENE NDIDZAFUNE KUKHALA ndiye wandituma kwa inu.’”+

  • Ekisodo 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+

  • 1 Mafumu 18:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Ndiyankheni Yehova, ndiyankheni, kuti anthu awa adziwe kuti inu Yehova+ ndinu Mulungu woona, ndiponso kuti mwabweza mitima yawo.”+

  • 2 Mafumu 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Tsopano inu Yehova Mulungu wathu,+ chonde tipulumutseni+ m’manja mwake, kuti maufumu onse a padziko lapansi adziwe kuti inu Yehova, inu nokha ndiye Mulungu.”+

  • Salimo 83:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+

      Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena