Yobu 38:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene nyenyezi za m’mawa+ zinafuula pamodzi mokondwera,Ndiponso pamene ana onse a Mulungu+ anayamba kufuula ndi chisangalalo? Salimo 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 M’patseni Yehova, inu amphamvu,*M’patseni Yehova ulemerero ndipo vomerezani kuti iye ndi wamphamvu.+
7 Pamene nyenyezi za m’mawa+ zinafuula pamodzi mokondwera,Ndiponso pamene ana onse a Mulungu+ anayamba kufuula ndi chisangalalo?
29 M’patseni Yehova, inu amphamvu,*M’patseni Yehova ulemerero ndipo vomerezani kuti iye ndi wamphamvu.+