Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno ana a Mulungu+ woona anayamba kuona+ kuti ana aakazi a anthu anali okongola. Chotero, anayamba kudzitengera okha akazi alionse amene anawasankha.

  • 1 Mafumu 22:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mikaya anapitiriza kunena kuti: “Choncho imvani mawu a Yehova:+ Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu,+ makamu onse akumwamba ataimirira kudzanja lake lamanja ndi kumanzere kwake.+

  • Yobu 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano linafika tsiku limene ana a Mulungu woona+ ankapita kukaonekera pamaso pa Yehova,+ ndipo ngakhalenso Satana+ anapita nawo limodzi.+

  • Yobu 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pambuyo pa zimenezi, linafika tsiku limene ana a Mulungu woona ankapita kukaonekera pamaso pa Yehova, ndipo nayenso Satana anapita nawo limodzi kukaonekera pamaso pa Yehova.+

  • Salimo 89:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Pakuti ndani kumwamba angayerekezeredwe ndi Yehova?+

      Ndani angafanane ndi Yehova pakati pa ana a Mulungu?+

  • Salimo 104:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Inu mumapanga angelo anu kukhala mizimu,+

      Ndipo atumiki anu kukhala moto wonyeketsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena