Zekariya 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Mulungu anandionetsa Yoswa+ mkulu wa ansembe, ataimirira pamaso pa mngelo wa Yehova. Pa nthawiyi Satana+ anali ataimirira kudzanja lamanja la Yoswa kuti azim’tsutsa.+ Mateyu 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Woyesayo+ anabwera n’kumuuza kuti: “Ngati ndinudi mwana wa Mulungu,+ uzani miyala iyi kuti isanduke mitanda ya mkate.” Luka 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Simoni, Simoni! Ndithu Satana+ akufuna anthu inu, kuti akupeteni ngati tirigu.+ Yohane 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chakudya chamadzulo chili mkati, Mdyerekezi anali ataika kale maganizo ofuna kupereka Yesu+ mumtima mwa Yudasi Isikariyoti,+ mwana wa Simoni. Chivumbulutso 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho chinjokacho+ chinaponyedwa pansi, njoka yakale ija,+ iye wotchedwa Mdyerekezi+ ndi Satana,+ amene akusocheretsa dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu. Iye anaponyedwa kudziko lapansi,+ ndipo angelo akenso anaponyedwa naye limodzi.
3 Ndiyeno Mulungu anandionetsa Yoswa+ mkulu wa ansembe, ataimirira pamaso pa mngelo wa Yehova. Pa nthawiyi Satana+ anali ataimirira kudzanja lamanja la Yoswa kuti azim’tsutsa.+
3 Ndiyeno Woyesayo+ anabwera n’kumuuza kuti: “Ngati ndinudi mwana wa Mulungu,+ uzani miyala iyi kuti isanduke mitanda ya mkate.”
2 Chakudya chamadzulo chili mkati, Mdyerekezi anali ataika kale maganizo ofuna kupereka Yesu+ mumtima mwa Yudasi Isikariyoti,+ mwana wa Simoni.
9 Choncho chinjokacho+ chinaponyedwa pansi, njoka yakale ija,+ iye wotchedwa Mdyerekezi+ ndi Satana,+ amene akusocheretsa dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu. Iye anaponyedwa kudziko lapansi,+ ndipo angelo akenso anaponyedwa naye limodzi.