Amosi 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti taonani, ine ndalamula kuti nyumba ya Isiraeli igwedezedwe pakati pa mitundu yonse,+ monga mmene munthu amachitira posefa, ndipo mwala sudzadutsa kuti ugwere pansi. Mateyu 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa ndi kundisiya ndekha usiku uno, pakuti Malemba amati, ‘Ndidzapha m’busa, ndipo nkhosa za m’gululo zidzabalalika.’+ Maliko 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa kundisiya ndekha, chifukwa Malemba amati, ‘Ndidzapha m’busa,+ ndipo nkhosa zidzabalalika.’+
9 Pakuti taonani, ine ndalamula kuti nyumba ya Isiraeli igwedezedwe pakati pa mitundu yonse,+ monga mmene munthu amachitira posefa, ndipo mwala sudzadutsa kuti ugwere pansi.
31 Kenako Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa ndi kundisiya ndekha usiku uno, pakuti Malemba amati, ‘Ndidzapha m’busa, ndipo nkhosa za m’gululo zidzabalalika.’+
27 Tsopano Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa kundisiya ndekha, chifukwa Malemba amati, ‘Ndidzapha m’busa,+ ndipo nkhosa zidzabalalika.’+