Mateyu 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa ndi kundisiya ndekha usiku uno, pakuti Malemba amati, ‘Ndidzapha m’busa, ndipo nkhosa za m’gululo zidzabalalika.’+ Mateyu 26:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Koma zonsezi zachitika kuti malemba a aneneri akwaniritsidwe.”+ Kenako ophunzira ake onse anamuthawa, n’kumusiya yekha.+ Maliko 14:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Pamenepo ophunzira ake onse anathawa ndi kumusiya+ yekha.+ Yohane 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Taonani! Nthawi ikubwera, ndipo yafika kale. Mubalalika aliyense kupita kunyumba kwake,+ ndipo mundisiya ndekha. Koma sindikhala ndekha, chifukwa Atate ali ndi ine.+
31 Kenako Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa ndi kundisiya ndekha usiku uno, pakuti Malemba amati, ‘Ndidzapha m’busa, ndipo nkhosa za m’gululo zidzabalalika.’+
56 Koma zonsezi zachitika kuti malemba a aneneri akwaniritsidwe.”+ Kenako ophunzira ake onse anamuthawa, n’kumusiya yekha.+
32 Taonani! Nthawi ikubwera, ndipo yafika kale. Mubalalika aliyense kupita kunyumba kwake,+ ndipo mundisiya ndekha. Koma sindikhala ndekha, chifukwa Atate ali ndi ine.+