Zekariya 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Iwe lupanga, nyamuka ukanthe m’busa wanga.+ Ukanthe mwamuna wamphamvu yemwe ndi mnzanga,”+ watero Yehova wa makamu. “Ipha m’busa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+ Ine ndidzakomera mtima nkhosa zonyozeka.”+ Maliko 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa kundisiya ndekha, chifukwa Malemba amati, ‘Ndidzapha m’busa,+ ndipo nkhosa zidzabalalika.’+ Yohane 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Taonani! Nthawi ikubwera, ndipo yafika kale. Mubalalika aliyense kupita kunyumba kwake,+ ndipo mundisiya ndekha. Koma sindikhala ndekha, chifukwa Atate ali ndi ine.+
7 “Iwe lupanga, nyamuka ukanthe m’busa wanga.+ Ukanthe mwamuna wamphamvu yemwe ndi mnzanga,”+ watero Yehova wa makamu. “Ipha m’busa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+ Ine ndidzakomera mtima nkhosa zonyozeka.”+
27 Tsopano Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa kundisiya ndekha, chifukwa Malemba amati, ‘Ndidzapha m’busa,+ ndipo nkhosa zidzabalalika.’+
32 Taonani! Nthawi ikubwera, ndipo yafika kale. Mubalalika aliyense kupita kunyumba kwake,+ ndipo mundisiya ndekha. Koma sindikhala ndekha, chifukwa Atate ali ndi ine.+