Miyambo 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ine ndinali pambali pake monga mmisiri waluso.+ Tsiku ndi tsiku, iye anali kusangalala kwambiri ndi ine.+ Ineyo ndinkakhala wosangalala pamaso pake nthawi zonse.+ Yohane 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pa chiyambi,+ panali wina wotchedwa Mawu,+ ndipo Mawuyo anali ndi Mulungu,+ komanso Mawuyo anali mulungu.*+ Yohane 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndinachokera kwa Atate ndipo ndinabwera m’dziko. Tsopano ndikuchoka m’dziko kupita kwa Atate.”+ Yohane 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo tsopano Atate, ndiloleni kuti ndikhale pambali panu, ndipo mundipatse ulemerero umene ndinali nawo pambali panu dziko lisanakhalepo.+
30 ine ndinali pambali pake monga mmisiri waluso.+ Tsiku ndi tsiku, iye anali kusangalala kwambiri ndi ine.+ Ineyo ndinkakhala wosangalala pamaso pake nthawi zonse.+
1 Pa chiyambi,+ panali wina wotchedwa Mawu,+ ndipo Mawuyo anali ndi Mulungu,+ komanso Mawuyo anali mulungu.*+
5 Ndipo tsopano Atate, ndiloleni kuti ndikhale pambali panu, ndipo mundipatse ulemerero umene ndinali nawo pambali panu dziko lisanakhalepo.+