1 Mafumu 8:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 inuyo mumve muli kumwamba, malo anu okhala okhazikika.+ Mumve pemphero lawo ndi pempho lawo lopempha chifundo, ndipo muonetsetse kuti chilungamo chachitika kwa iwo.+ Salimo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+Yehova, mpando wake wachifumu uli kumwamba.+Maso ake amaona, maso ake owala amasanthula+ ana a anthu. Yohane 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yesu anali kudziwa kuti Atate anapereka zinthu zonse m’manja mwake.+ Analinso kudziwa kuti anabwera kuchokera kwa Mulungu ndi kuti anali kupita kwa Mulungu.+ Aheberi 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti Khristu sanalowe m’malo oyera amkatikati opangidwa ndi manja a anthu,+ amene ndi chithunzi cha malo enieniwo,+ koma analowa kumwamba kwenikweniko.+ Tsopano ali kumwamba kuti aonekere pamaso pa Mulungu chifukwa cha ife.+
49 inuyo mumve muli kumwamba, malo anu okhala okhazikika.+ Mumve pemphero lawo ndi pempho lawo lopempha chifundo, ndipo muonetsetse kuti chilungamo chachitika kwa iwo.+
4 Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+Yehova, mpando wake wachifumu uli kumwamba.+Maso ake amaona, maso ake owala amasanthula+ ana a anthu.
3 Yesu anali kudziwa kuti Atate anapereka zinthu zonse m’manja mwake.+ Analinso kudziwa kuti anabwera kuchokera kwa Mulungu ndi kuti anali kupita kwa Mulungu.+
24 Pakuti Khristu sanalowe m’malo oyera amkatikati opangidwa ndi manja a anthu,+ amene ndi chithunzi cha malo enieniwo,+ koma analowa kumwamba kwenikweniko.+ Tsopano ali kumwamba kuti aonekere pamaso pa Mulungu chifukwa cha ife.+