2 Mbiri 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 n’kunena kuti:+ “Inu Yehova Mulungu wa makolo athu,+ kodi si inu Mulungu wakumwamba?+ Kodi inu simukulamulira maufumu onse a mitundu ya anthu?+ Kodi m’dzanja lanu si muli mphamvu kotero kuti palibe amene angalimbane nanu?+ Salimo 103:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova wakhazikitsa mpando wake wachifumu kumwamba.+Ndipo ufumu wake ukulamulira chilichonse.+ Mateyu 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Wolumbirira kumwamba walumbirira mpando wachifumu wa Mulungu+ komanso amene akukhala pampandowo. Machitidwe 7:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 ‘Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi inu mudzandimangira nyumba yotani? akutero Yehova. Kapena malo oti ine ndipumuliremo ali kuti?+ Chivumbulutso 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zitatero, nthawi yomweyo ndinakhala mumphamvu ya mzimu, ndipo mpando wachifumu+ unaoneka uli pamalo ake kumwamba,+ wina atakhalapo.+
6 n’kunena kuti:+ “Inu Yehova Mulungu wa makolo athu,+ kodi si inu Mulungu wakumwamba?+ Kodi inu simukulamulira maufumu onse a mitundu ya anthu?+ Kodi m’dzanja lanu si muli mphamvu kotero kuti palibe amene angalimbane nanu?+
49 ‘Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi inu mudzandimangira nyumba yotani? akutero Yehova. Kapena malo oti ine ndipumuliremo ali kuti?+
2 Zitatero, nthawi yomweyo ndinakhala mumphamvu ya mzimu, ndipo mpando wachifumu+ unaoneka uli pamalo ake kumwamba,+ wina atakhalapo.+