Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 16:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pajatu maso a Yehova+ akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake kwa anthu amene mtima wawo+ uli wathunthu kwa iye. Mwachita zopusa+ pankhani imeneyi, chifukwa kuyambira tsopano anthu azichita nanu nkhondo.”+

  • Salimo 33:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kuchokera kumwamba, Yehova wayang’ana,+

      Waona ana onse a anthu.+

  • Salimo 66:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Iye akulamulira ndi mphamvu zake mpaka kalekale.+

      Maso ake akuyang’anitsitsa mitundu ya anthu.+

      Koma anthu oumitsa khosi asadzikweze.+ [Seʹlah.]

  • Miyambo 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Maso a Yehova ali paliponse.+ Amayang’ana anthu oipa ndi abwino omwe.+

  • Zekariya 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Munthu asakunyozeni chifukwa chakuti munayamba kumanga ndi zinthu zochepa.+ Anthu adzasangalala ndi ntchito imeneyi+ ndipo adzaona chingwe cha mmisiri womanga nyumba m’dzanja la Zerubabele. Maso 7 adzaona zimenezi. Maso 7 amenewa ndiwo maso a Yehova,+ ndipo akuyang’ana uku ndi uku padziko lonse lapansi.”+

  • Aheberi 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena