-
Zekariya 4:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Munthu asakunyozeni chifukwa chakuti munayamba kumanga ndi zinthu zochepa.+ Anthu adzasangalala ndi ntchito imeneyi+ ndipo adzaona chingwe cha mmisiri womanga nyumba m’dzanja la Zerubabele. Maso 7 adzaona zimenezi. Maso 7 amenewa ndiwo maso a Yehova,+ ndipo akuyang’ana uku ndi uku padziko lonse lapansi.”+
-