Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ansembe+ ndi Alevi ambiri, omwe anali atsogoleri a nyumba za makolo awo,+ amuna okalamba amene anaona nyumba yoyambirira,+ anali kulira+ mokweza chifukwa cha kumangidwa kwa maziko+ a nyumbayo pamaso pawo, ndipo enanso ambiri anali kufuula mosangalala.+

  • Hagai 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 ‘Kodi pakati panu pali wotsala aliyense amene anaona ulemerero umene nyumbayi inali nawo poyamba?+ Kodi panopa mukuiona bwanji? Kodi simukuona kuti ilibe ulemerero poyerekeza ndi ulemerero umene inali nawo poyamba?’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena