1 Mafumu 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nyumba yonseyo anaikuta ndi golide+ mpaka kuimaliza, ndipo guwa lansembe lonse,+ lomwe linali kufupi ndi chipinda chamkati, analikuta ndi golide.+ Hagai 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ‘Kodi pakati panu pali wotsala aliyense amene anaona ulemerero umene nyumbayi inali nawo poyamba?+ Kodi panopa mukuiona bwanji? Kodi simukuona kuti ilibe ulemerero poyerekeza ndi ulemerero umene inali nawo poyamba?’+
22 Nyumba yonseyo anaikuta ndi golide+ mpaka kuimaliza, ndipo guwa lansembe lonse,+ lomwe linali kufupi ndi chipinda chamkati, analikuta ndi golide.+
3 ‘Kodi pakati panu pali wotsala aliyense amene anaona ulemerero umene nyumbayi inali nawo poyamba?+ Kodi panopa mukuiona bwanji? Kodi simukuona kuti ilibe ulemerero poyerekeza ndi ulemerero umene inali nawo poyamba?’+