2 Mbiri 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo mitanda yake ya denga,* makomo, makoma,* ndi zitseko za nyumbayo anazikuta ndi golide.+ Pamakoma ake anajambulapo akerubi mochita kugoba.+
7 Ndipo mitanda yake ya denga,* makomo, makoma,* ndi zitseko za nyumbayo anazikuta ndi golide.+ Pamakoma ake anajambulapo akerubi mochita kugoba.+