Ekisodo 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Ndiyeno upange chihema chopatulika ndi nsalu 10 zopangira hema.+ Nsaluzo zikhale zaulusi wopota wabwino kwambiri, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira+ ndi ulusi wofiira kwambiri. Pansaluzo upetepo akerubi.+ 1 Mafumu 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamakoma onse a nyumbayo, m’zipinda zonse ziwiri, chamkati ndi chakunja, anajambulapo akerubi,+ mitengo ya kanjedza,+ ndi maluwa.+ Anajambula zinthu zimenezi mochita kugoba.
26 “Ndiyeno upange chihema chopatulika ndi nsalu 10 zopangira hema.+ Nsaluzo zikhale zaulusi wopota wabwino kwambiri, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira+ ndi ulusi wofiira kwambiri. Pansaluzo upetepo akerubi.+
29 Pamakoma onse a nyumbayo, m’zipinda zonse ziwiri, chamkati ndi chakunja, anajambulapo akerubi,+ mitengo ya kanjedza,+ ndi maluwa.+ Anajambula zinthu zimenezi mochita kugoba.