2 Mafumu 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Hezekiya anayamba kupemphera+ pamaso pa Yehova, kuti: “Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli+ wokhala pa akerubi,+ inu nokha ndinu Mulungu woona wa maufumu onse+ a padziko lapansi.+ Inuyo munapanga kumwamba+ ndi dziko lapansi.+ 2 Mbiri 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anapanganso nsalu yotchinga+ ya ulusi wabuluu,+ ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira ndi nsalu yofiira komanso yabwino kwambiri. Kenako nsaluyo anaikongoletsa ndi akerubi.+
15 Ndiyeno Hezekiya anayamba kupemphera+ pamaso pa Yehova, kuti: “Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli+ wokhala pa akerubi,+ inu nokha ndinu Mulungu woona wa maufumu onse+ a padziko lapansi.+ Inuyo munapanga kumwamba+ ndi dziko lapansi.+
14 Anapanganso nsalu yotchinga+ ya ulusi wabuluu,+ ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira ndi nsalu yofiira komanso yabwino kwambiri. Kenako nsaluyo anaikongoletsa ndi akerubi.+