2 Mbiri 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma mfumu Hezekiya+ ndi mneneri+ Yesaya+ mwana wa Amozi,+ anali kupempherera nkhani imeneyi+ ndi kufuulira Mulungu kumwamba kuti awapulumutse.+ Danieli 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinayang’ana+ kwa Yehova Mulungu woona kuti ndimufunefune mwa kupemphera,+ kumuchonderera, kusala kudya, kuvala ziguduli* ndi kudzithira phulusa.+ Afilipi 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Musamade nkhawa ndi kanthu kalikonse,+ koma pa chilichonse, mwa pemphero ndi pembedzero,+ pamodzi ndi chiyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.+
20 Koma mfumu Hezekiya+ ndi mneneri+ Yesaya+ mwana wa Amozi,+ anali kupempherera nkhani imeneyi+ ndi kufuulira Mulungu kumwamba kuti awapulumutse.+
3 Ndinayang’ana+ kwa Yehova Mulungu woona kuti ndimufunefune mwa kupemphera,+ kumuchonderera, kusala kudya, kuvala ziguduli* ndi kudzithira phulusa.+
6 Musamade nkhawa ndi kanthu kalikonse,+ koma pa chilichonse, mwa pemphero ndi pembedzero,+ pamodzi ndi chiyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.+