2 Mafumu 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso, inatuma Eliyakimu+ amene anali woyang’anira banja la mfumu, Sebina+ mlembi, ndi akuluakulu a ansembe, onse atavala ziguduli, kuti apite kwa mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi.+
2 Komanso, inatuma Eliyakimu+ amene anali woyang’anira banja la mfumu, Sebina+ mlembi, ndi akuluakulu a ansembe, onse atavala ziguduli, kuti apite kwa mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi.+