Yesaya 37:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso inatuma Eliyakimu+ amene anali woyang’anira banja la mfumu, Sebina mlembi,+ ndi akuluakulu a ansembe,+ onse atavala ziguduli, kuti apite kwa mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi.+
2 Komanso inatuma Eliyakimu+ amene anali woyang’anira banja la mfumu, Sebina mlembi,+ ndi akuluakulu a ansembe,+ onse atavala ziguduli, kuti apite kwa mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi.+