2 Mbiri 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nkhani zina zokhudza Uziya,+ zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa ndi mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi.+ Luka 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anali kuchita zimenezi monga mmene analembera m’buku la mawu a Yesaya mneneri kuti: “Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani njira ya Yehova anthu inu! Wongolani misewu yake.+
22 Nkhani zina zokhudza Uziya,+ zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa ndi mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi.+
4 Anali kuchita zimenezi monga mmene analembera m’buku la mawu a Yesaya mneneri kuti: “Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani njira ya Yehova anthu inu! Wongolani misewu yake.+