Genesis 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pa chiyambi,+ Mulungu+ analenga+ kumwamba ndi dziko lapansi.+ Salimo 96:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake,+Koma Yehova ndiye anapanga kumwamba.+ Salimo 102:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munaika kalekale maziko a dziko lapansi,+Ndipo kumwamba ndiko ntchito ya manja anu.+ Yohane 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zinthu zonse zinakhalako kudzera mwa iye,+ ndipo palibe chinthu ngakhale chimodzi chimene chinakhalapo popanda iyeyo.
5 Chifukwa milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake,+Koma Yehova ndiye anapanga kumwamba.+
3 Zinthu zonse zinakhalako kudzera mwa iye,+ ndipo palibe chinthu ngakhale chimodzi chimene chinakhalapo popanda iyeyo.