Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 16:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Chifukwa milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake.+

      Koma Yehova, ndiye anapanga kumwamba.+

  • Salimo 97:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Onse amene akupembedza chifaniziro chilichonse achite manyazi.+

      Amene amadzitama chifukwa cha milungu yopanda pake achite manyazi.+

      Muweramireni, inu milungu yonse.+

  • Yesaya 37:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Atentha milungu yawo pamoto,+ chifukwa sinali milungu,+ koma ntchito ya manja a anthu,+ mitengo ndi miyala, n’chifukwa chake anaiwononga.+

  • Yesaya 44:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kwa aliyense amene wapanga mulungu kapena kuumba fano lopangidwa ndi chitsulo chosungunula,+ lidzakhala lopanda phindu ngakhale pang’ono.+

  • Yeremiya 10:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mitunduyo mukaiuze izi anthu inu: “Milungu+ imene sinapange kumwamba ndi dziko lapansi+ ndi imene idzawonongedwe padziko lapansi, pansi pa thambo.”

  • 1 Akorinto 8:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena