Deuteronomo 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tamverani, Aisiraeli inu: Yehova Mulungu wathu ndi Yehova mmodzi.*+ Deuteronomo 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+Ndipo palibe milungu ina pamodzi ndi ine.+Ndimapha ndiponso ndimapereka moyo.+Ndavulaza koopsa,+ ndipo ine ndidzachiritsa,+Palibe aliyense wonditsomphola m’dzanja langa.+ Aefeso 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ndi Mulungu mmodzi+ amenenso ndi Atate wa anthu onse. Iye ali pamwamba pa onse ndipo amachita zinthu kudzera mwa onse ndiponso mphamvu yake imagwira ntchito mwa onse.
39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+Ndipo palibe milungu ina pamodzi ndi ine.+Ndimapha ndiponso ndimapereka moyo.+Ndavulaza koopsa,+ ndipo ine ndidzachiritsa,+Palibe aliyense wonditsomphola m’dzanja langa.+
6 ndi Mulungu mmodzi+ amenenso ndi Atate wa anthu onse. Iye ali pamwamba pa onse ndipo amachita zinthu kudzera mwa onse ndiponso mphamvu yake imagwira ntchito mwa onse.