7 Mfumu ya Isiraeli itawerenga kalatayo, nthawi yomweyo inang’amba+ zovala zake n’kunena kuti: “Kodi ine ndine Mulungu,+ wotha kupha munthu kapena kum’siya wamoyo?+ Munthu uyu wanditumizira wodwala kuti ndim’chiritse khate lake. Taonani amuna inu kuti munthuyu akufuna kukangana nane.”+