Yobu 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zikanakhala bwino mukanandibisa m’Manda,+Mukanandibisa mpaka mkwiyo wanu utachoka,Mukanati mundiikire nthawi+ n’kudzandikumbukira.+ Salimo 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, mwanditulutsa m’Manda,+Mwandisunga ndi moyo, kuti ndisatsikire m’dzenje.+ Salimo 49:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Mulungu adzawombola moyo wanga ku Manda,+Pakuti adzandilandira. [Seʹlah.] Salimo 86:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene mwandisonyeza ndi kwakukulu,+Ndipo mwapulumutsa moyo wanga ku Manda, kumalo apansi penipeni.+ Yohane 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Marita anati: “Ndikudziwa kuti adzauka pa kuuka kwa akufa+ m’tsiku lomaliza.” 1 Akorinto 15:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 “Imfa iwe, kupambana kwako kuli kuti? Imfawe, mphamvu yako ili kuti?”+
13 Zikanakhala bwino mukanandibisa m’Manda,+Mukanandibisa mpaka mkwiyo wanu utachoka,Mukanati mundiikire nthawi+ n’kudzandikumbukira.+
13 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene mwandisonyeza ndi kwakukulu,+Ndipo mwapulumutsa moyo wanga ku Manda, kumalo apansi penipeni.+