Genesis 44:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiye ngati uyunso mungapite naye, iye n’kukakumana ndi tsoka n’kufa, ndithu mudzatsitsira ku Manda+ imvi zangazi ndi chisoni.’ 1 Samueli 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova ndi Wakupha ndi Wosunga moyo,+Iye ndi Wotsitsira Kumanda,+ ndiponso Woukitsa.+ Yesaya 57:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye amalowa mumtendere.+ Aliyense woyenda mowongoka+ amapita kukapuma+ m’manda.*+
29 Ndiye ngati uyunso mungapite naye, iye n’kukakumana ndi tsoka n’kufa, ndithu mudzatsitsira ku Manda+ imvi zangazi ndi chisoni.’