Danieli 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Iye amaona anthu onse okhala padziko lapansi ngati opanda pake+ ndipo amachita zinthu mogwirizana ndi chifuniro chake pakati pa makamu akumwamba ndi pakati pa anthu okhala padziko lapansi.+ Palibe aliyense amene angaletse dzanja+ lake kapena kumufunsa kuti, ‘Mukuchita chiyani?’+ Machitidwe 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu+ mokweza mawu kuti: “Ambuye Wamkulu Koposa,+ Inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zokhala mmenemo.+
35 Iye amaona anthu onse okhala padziko lapansi ngati opanda pake+ ndipo amachita zinthu mogwirizana ndi chifuniro chake pakati pa makamu akumwamba ndi pakati pa anthu okhala padziko lapansi.+ Palibe aliyense amene angaletse dzanja+ lake kapena kumufunsa kuti, ‘Mukuchita chiyani?’+
24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu+ mokweza mawu kuti: “Ambuye Wamkulu Koposa,+ Inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zokhala mmenemo.+