Yeremiya 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndichiritseni inu Yehova, ndipo ndidzachiradi.+ Ndipulumutseni ndipo ndidzapulumukadi,+ pakuti ine ndimatamanda inu.+ Hoseya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Bwerani anthu inu. Tiyeni tibwerere kwa Yehova,+ pakuti iye watikhadzulakhadzula+ koma adzatichiritsa.+ Wakhala akutivulaza koma adzamanga zilonda zathu.+
14 Ndichiritseni inu Yehova, ndipo ndidzachiradi.+ Ndipulumutseni ndipo ndidzapulumukadi,+ pakuti ine ndimatamanda inu.+
6 “Bwerani anthu inu. Tiyeni tibwerere kwa Yehova,+ pakuti iye watikhadzulakhadzula+ koma adzatichiritsa.+ Wakhala akutivulaza koma adzamanga zilonda zathu.+