Yesaya 55:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu woipa asiye njira yake+ ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.+ Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+ Abwerere kwa Mulungu wathu, pakuti amakhululuka ndi mtima wonse.+ Yeremiya 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Bwererani, inu ana opanduka.+ Ndidzachiritsa kusakhulupirika kwanu.”+ “Ife tabwerera! Tabwera kwa inu, pakuti inu Yehova ndinu Mulungu wathu.+
7 Munthu woipa asiye njira yake+ ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.+ Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+ Abwerere kwa Mulungu wathu, pakuti amakhululuka ndi mtima wonse.+
22 “Bwererani, inu ana opanduka.+ Ndidzachiritsa kusakhulupirika kwanu.”+ “Ife tabwerera! Tabwera kwa inu, pakuti inu Yehova ndinu Mulungu wathu.+