Numeri 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Mose anayamba kufuulira Yehova kuti: “Chonde Mulungu wanga! M’chiritseni chonde!”+ 2 Mbiri 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pambuyo pa zonsezi, Yehova anamudwalitsa matenda a m’matumbo osachiritsika.+