2 Mbiri 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anapanganso katani*+ pogwiritsa ntchito ulusi wabuluu, ubweya wapepo, nsalu yofiira ndi nsalu yabwino kwambiri. Kenako anajambulapo akerubi.+
14 Iye anapanganso katani*+ pogwiritsa ntchito ulusi wabuluu, ubweya wapepo, nsalu yofiira ndi nsalu yabwino kwambiri. Kenako anajambulapo akerubi.+