2 Mbiri 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anapanganso nsalu yotchinga+ ya ulusi wabuluu,+ ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira ndi nsalu yofiira komanso yabwino kwambiri. Kenako nsaluyo anaikongoletsa ndi akerubi.+
14 Anapanganso nsalu yotchinga+ ya ulusi wabuluu,+ ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira ndi nsalu yofiira komanso yabwino kwambiri. Kenako nsaluyo anaikongoletsa ndi akerubi.+