Mateyu 27:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Nthawi yomweyo nsalu yotchinga yamʼnyumba yopatulika+ inangʼambika pakati+ kuchokera pamwamba mpaka pansi.+ Dziko lapansi linagwedezeka ndipo matanthwe anangʼambika. Aheberi 10:19, 20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho abale, timalimba mtima kulowa mʼmalo oyera+ chifukwa cha magazi a Yesu. 20 Iye ndi amene anatitsegulira njira imeneyi yomwe ndi yatsopano komanso yamoyo ndipo imadutsa katani yotchingira,+ imene ndi thupi lake.
51 Nthawi yomweyo nsalu yotchinga yamʼnyumba yopatulika+ inangʼambika pakati+ kuchokera pamwamba mpaka pansi.+ Dziko lapansi linagwedezeka ndipo matanthwe anangʼambika.
19 Choncho abale, timalimba mtima kulowa mʼmalo oyera+ chifukwa cha magazi a Yesu. 20 Iye ndi amene anatitsegulira njira imeneyi yomwe ndi yatsopano komanso yamoyo ndipo imadutsa katani yotchingira,+ imene ndi thupi lake.