Genesis 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chotero anam’pitikitsa munthuyo. Ndiyeno anaika akerubi+ kum’mawa kwa munda wa Edeniwo.+ Anaikanso lupanga loyaka moto, limene linali kuzungulira mosalekeza, kutchinga njira yopita ku mtengo wa moyo. Salimo 99:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 99 Yehova wakhala mfumu.+ Mitundu ya anthu inthunthumire.+Iye wakhala pa akerubi.+ Ndipo dziko lapansi linjenjemere.+
24 Chotero anam’pitikitsa munthuyo. Ndiyeno anaika akerubi+ kum’mawa kwa munda wa Edeniwo.+ Anaikanso lupanga loyaka moto, limene linali kuzungulira mosalekeza, kutchinga njira yopita ku mtengo wa moyo.
99 Yehova wakhala mfumu.+ Mitundu ya anthu inthunthumire.+Iye wakhala pa akerubi.+ Ndipo dziko lapansi linjenjemere.+