Genesis 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova Mulungu atatero, anakonza munda ku Edeni,+ chakum’mawa, ndipo m’mundamo anaikamo munthu amene anamuumbayo.+ Genesis 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamenepo Kaini anachoka pamaso pa Yehova+ n’kupita kukakhala kudera la kum’mawa kwa Edeni monga wothawa.
8 Yehova Mulungu atatero, anakonza munda ku Edeni,+ chakum’mawa, ndipo m’mundamo anaikamo munthu amene anamuumbayo.+
16 Pamenepo Kaini anachoka pamaso pa Yehova+ n’kupita kukakhala kudera la kum’mawa kwa Edeni monga wothawa.