Genesis 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Kaini anachoka pamaso pa Yehova nʼkupita kukakhala kudera la Nodi,* kumʼmawa kwa Edeni.+