Genesis 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamenepo Kaini anachoka pamaso pa Yehova+ n’kupita kukakhala kudera la kum’mawa kwa Edeni monga wothawa.
16 Pamenepo Kaini anachoka pamaso pa Yehova+ n’kupita kukakhala kudera la kum’mawa kwa Edeni monga wothawa.