Ekisodo 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Upange chihema+ pogwiritsa ntchito nsalu 10 zopangira tenti. Nsaluzo zikhale za ulusi wopota wabwino kwambiri, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo ndi ulusi wofiira kwambiri. Pansaluzo upetepo+ akerubi.+
26 “Upange chihema+ pogwiritsa ntchito nsalu 10 zopangira tenti. Nsaluzo zikhale za ulusi wopota wabwino kwambiri, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo ndi ulusi wofiira kwambiri. Pansaluzo upetepo+ akerubi.+