Genesis 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho anathamangitsa munthuyo mʼmundamo, nʼkuika akerubi+ kumʼmawa kwa munda wa Edeniwo. Anaikanso lupanga loyaka moto, limene linkazungulira nthawi zonse, kutchinga njira yopita kumtengo wa moyo. Salimo 99:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 99 Yehova wakhala Mfumu.+ Mitundu ya anthu injenjemere. Iye wakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi.+ Dziko lapansi ligwedezeke.
24 Choncho anathamangitsa munthuyo mʼmundamo, nʼkuika akerubi+ kumʼmawa kwa munda wa Edeniwo. Anaikanso lupanga loyaka moto, limene linkazungulira nthawi zonse, kutchinga njira yopita kumtengo wa moyo.
99 Yehova wakhala Mfumu.+ Mitundu ya anthu injenjemere. Iye wakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi.+ Dziko lapansi ligwedezeke.