Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 40:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Zipinda za alondazo komanso zipilala zimene zinali m’mbali mwa zipindazo zinali ndi mawindo okhala ndi mafelemu aakulu mkati koma aang’ono kunja+ kuzungulira kanyumba konseko. Umu ndi mmenenso zinalili ndi mawindo apakhonde. Mkati mwa kanyumbako munali mawindo aakulu mkati, kuzungulira mbali zonse ndipo pazipilala zam’mbali panali zithunzi za mtengo wa kanjedza.+

  • Ezekieli 41:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ngakhalenso zithunzi zojambula mochita kugoba za akerubi+ ndi za mitengo ya kanjedza,+ zinali ndi miyezo yake. Mitengoyo inali pakati pa kerubi ndi kerubi mnzake, ndipo akerubiwo anali ndi nkhope ziwiriziwiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena