Ezekieli 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kerubi aliyense anali ndi nkhope zinayi.+ Nkhope yoyamba inali ya kerubi. Nkhope yachiwiri inali ya munthu.+ Nkhope yachitatu inali ya mkango, ndipo nkhope yachinayi inali ya chiwombankhanga.+
14 Kerubi aliyense anali ndi nkhope zinayi.+ Nkhope yoyamba inali ya kerubi. Nkhope yachiwiri inali ya munthu.+ Nkhope yachitatu inali ya mkango, ndipo nkhope yachinayi inali ya chiwombankhanga.+