Ezekieli 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ponena za maonekedwe a nkhope zawo, zamoyo zinayi zimenezi zinali ndi nkhope ya munthu,+ nkhope ya mkango+ mbali ya kumanja,+ nkhope ya ng’ombe yamphongo+ mbali ya kumanzere,+ ndiponso nkhope ya chiwombankhanga.+ Chivumbulutso 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chamoyo choyamba chinali ngati mkango.+ Chamoyo chachiwiri chinali ngati mwana wa ng’ombe wamphongo.+ Chamoyo+ chachitatu chinali ndi nkhope ngati ya munthu, ndipo chamoyo+ chachinayi chinali ngati chiwombankhanga+ chimene chikuuluka.
10 Ponena za maonekedwe a nkhope zawo, zamoyo zinayi zimenezi zinali ndi nkhope ya munthu,+ nkhope ya mkango+ mbali ya kumanja,+ nkhope ya ng’ombe yamphongo+ mbali ya kumanzere,+ ndiponso nkhope ya chiwombankhanga.+
7 Chamoyo choyamba chinali ngati mkango.+ Chamoyo chachiwiri chinali ngati mwana wa ng’ombe wamphongo.+ Chamoyo+ chachitatu chinali ndi nkhope ngati ya munthu, ndipo chamoyo+ chachinayi chinali ngati chiwombankhanga+ chimene chikuuluka.