Chivumbulutso 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atamatula+ chidindo chachitatu, ndinamva chamoyo chachitatu+ chikunena kuti: “Bwera!” Ndipo nditayang’ana, ndinaona hatchi yakuda. Wokwerapo wake anali ndi sikelo+ m’dzanja lake.
5 Atamatula+ chidindo chachitatu, ndinamva chamoyo chachitatu+ chikunena kuti: “Bwera!” Ndipo nditayang’ana, ndinaona hatchi yakuda. Wokwerapo wake anali ndi sikelo+ m’dzanja lake.