Yobu 39:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chimafunafuna chakudya kuchokera pamenepo.+Maso ake amaona kutali kwambiri. Miyambo 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Njira ya chiwombankhanga m’mlengalenga, njira ya njoka pamwala, njira ya ngalawa pakatikati pa nyanja,+ ndiponso njira ya mwamuna ndi mtsikana.+ Ezekieli 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kerubi aliyense anali ndi nkhope zinayi.+ Nkhope yoyamba inali ya kerubi. Nkhope yachiwiri inali ya munthu.+ Nkhope yachitatu inali ya mkango, ndipo nkhope yachinayi inali ya chiwombankhanga.+
19 Njira ya chiwombankhanga m’mlengalenga, njira ya njoka pamwala, njira ya ngalawa pakatikati pa nyanja,+ ndiponso njira ya mwamuna ndi mtsikana.+
14 Kerubi aliyense anali ndi nkhope zinayi.+ Nkhope yoyamba inali ya kerubi. Nkhope yachiwiri inali ya munthu.+ Nkhope yachitatu inali ya mkango, ndipo nkhope yachinayi inali ya chiwombankhanga.+