Chivumbulutso 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo ndinaona ndi kumva chiwombankhanga+ chikuuluka pafupi m’mlengalenga,+ chikulankhula ndi mawu okweza kuti: “Tsoka, tsoka, tsoka+ kwa okhala padziko lapansi, chifukwa cha malipenga otsalawo, amene angelo atatuwo atsala pang’ono kuwaliza!”+
13 Ndipo ndinaona ndi kumva chiwombankhanga+ chikuuluka pafupi m’mlengalenga,+ chikulankhula ndi mawu okweza kuti: “Tsoka, tsoka, tsoka+ kwa okhala padziko lapansi, chifukwa cha malipenga otsalawo, amene angelo atatuwo atsala pang’ono kuwaliza!”+