Yobu 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ayenda ngati ngalawa za bango,Ngati chiwombankhanga chimene chimauluka uku ndi uko pofunafuna chakudya.+ Yeremiya 49:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Taonani! Wina adzakwera kenako n’kutsika ngati chiwombankhanga chimene chikufuna kugwira chakudya chake.+ Adzatambasulira mapiko ake pa Bozira,+ ndipo pa tsikulo mtima wa amuna amphamvu a ku Edomu udzakhala ngati mtima wa mkazi amene akumva zowawa za pobereka.”+
26 Ayenda ngati ngalawa za bango,Ngati chiwombankhanga chimene chimauluka uku ndi uko pofunafuna chakudya.+
22 Taonani! Wina adzakwera kenako n’kutsika ngati chiwombankhanga chimene chikufuna kugwira chakudya chake.+ Adzatambasulira mapiko ake pa Bozira,+ ndipo pa tsikulo mtima wa amuna amphamvu a ku Edomu udzakhala ngati mtima wa mkazi amene akumva zowawa za pobereka.”+