Habakuku 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mahatchi* ake ndi aliwiro kuposa akambuku* ndiponso ndi oopsa kuposa mimbulu yoyenda usiku.+ Mahatchi ake ankhondo amachita mgugu ndipo amachokera kutali. Mahatchiwo amauluka ngati chiwombankhanga chimene chikuthamangira chakudya chake.+
8 Mahatchi* ake ndi aliwiro kuposa akambuku* ndiponso ndi oopsa kuposa mimbulu yoyenda usiku.+ Mahatchi ake ankhondo amachita mgugu ndipo amachokera kutali. Mahatchiwo amauluka ngati chiwombankhanga chimene chikuthamangira chakudya chake.+